Ezekieli 40:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi kunja kwa cipata ca m'kati kunali tinyumba ta oyimba m'bwalo lam'kati, ku mbali ya cipata ca kumpoto; ndipo tinaloza kumwela, kena ku mbali ya cipata ca kum'mawa kanaloza kumpoto.

Ezekieli 40

Ezekieli 40:41-47