Ezekieli 40:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

zipinda zace, makhoma a pakati pace, ndi zidundumwa zace; ndimo munali mazenera m'menemo pozungulirapo, m'litali mwace mikono makumi asanu, ndi kupingasa kwace mikono makumi awiri mphambu isanu.

Ezekieli 40

Ezekieli 40:27-39