Ezekieli 40:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi zidundumwa zace zinaloza ku bwalo lakunja, ndi pa nsanamira zace panali akanjedza, ndi pokwererapo panali makwerero asanu ndi atatu.

Ezekieli 40

Ezekieli 40:26-39