Ezekieli 40:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndimo munali mazenera m'menemo, ndi m'zidundumwa zace pozungulirapo, monga mazenera ena aja, m'litali mwace mikono makumi asanu, ndi kupingasa kwace mikono makumi awiri mphambu isanu.

Ezekieli 40

Ezekieli 40:16-33