Ezekieli 40:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anayesa kupingasa kwace kuyambira pakhomo pace pacipata cakunsi, kufikira kumaso kwace kwa bwalo la m'kati kunja kwace, mikono zana kum'mawa, ndi kumpoto.

Ezekieli 40

Ezekieli 40:17-23