Ezekieli 4:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nudzitengere ciwaya cacitsulo, ndi kuciika ngati khoma lacitsulo pakati pa iwe ndi mudziwo; nuulozetsere nkhope yako kuti umangidwire misasa, ndipo udzamangira misasa. Ici cikhale cizindikilo ca nyumba ya Israyeli.

Ezekieli 4

Ezekieli 4:1-11