Ezekieli 38:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Gomeri ndi magulu ace onse, nyumba ya Togarima, ku malekezero a kumpoto, ndi magulu ace onse, mitundu yambiri pamodzi ndi iwe.

Ezekieli 38

Ezekieli 38:5-10