Ezekieli 37:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinapenya, taonani, panali mitsempha pa iwo, panadzaponso mnofu, ndi khungu linawakuta pamwamba pace; koma munalibe mpweya mwa iwo.

Ezekieli 37

Ezekieli 37:3-16