Ezekieli 37:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzakuikirani mtsempha, ndi kufikitsira inu mnofu, ndi kukuta inu ndi khungu, ndi kulonga mpweya mwa inu; ndipo mudzakhala ndi moyo; motero mudzadziwa kuti Ine ndine Yehoya.

Ezekieli 37

Ezekieli 37:1-9