Ezekieli 37:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, mafupa awa nkukhala ndi moyo kodi? Ndipo ndinati, Ambuye Yehova, mudziwa ndinu.

Ezekieli 37

Ezekieli 37:1-7