Ezekieli 37:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzapangana nao pangano la mtendere, lidzakhala pangano losatha nao, ndipo ndidzawakhazika, ndi kuwacurukitsa, ndi kuika malo anga opatulika pakati pao kosatha.

Ezekieli 37

Ezekieli 37:17-28