Ezekieli 37:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yao, ndipo iwo onse adzakhala ndi mbusa mmodzi, adzayendanso m'maweruzo anga, nadzasunga malemba anga ndi kuwacita.

Ezekieli 37

Ezekieli 37:20-28