Ezekieli 37:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace, nenera, nunene nao, Atero Ambuye Yehova, Taonani anthu anga, ndidzatsegula kumanda kwanu, ndi kukweza inu muturuke m'manda mwanu, ndipo ndidzakulowetsani m'dziko la Israyeli.

Ezekieli 37

Ezekieli 37:2-18