Ezekieli 36:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma inu, mapiri a Israyeli, mudzaphukitsa nthambi zanu, ndi kubalira anthu anga Israyeli zipatso zanu, pakuti ayandikira kufika.

Ezekieli 36

Ezekieli 36:1-17