Ezekieli 36:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace unenere za dziko la Israyeli, nuti kwa mapiri ndi kwa zitunda, kwa mitsinje ndi kwa zigwa, Atero Ambuye Yehova, Taonani, ndalankhula mu nsanje yanga ndi ukali wanga, popeza mwasenza manyazi a amitundu;

Ezekieli 36

Ezekieli 36:4-12