Ezekieli 36:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzakupatsani mtima watsopano, ndi kulonga m'kati mwanu mzimu watsopano; ndipo ndidzacotsa mtima wamwala m'thupi, ndi kukupatsani mtima wamnofu.

Ezekieli 36

Ezekieli 36:17-30