Ezekieli 36:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wobadwa ndi munthu iwe, muja a nyumba ya Israyeli anakhala m'dziko mwao, analidetsa ndi njira yao, ndi macitidwe ao; njira yao pamaso panga inanga cidetso ca mkazi wooloka.

Ezekieli 36

Ezekieli 36:15-18