Ezekieli 35:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidzakusandutsa mabwinja osatha; ndi m'midzi mwako simudzakhalanso anthu; motero mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova,

Ezekieli 35

Ezekieli 35:2-12