Ezekieli 34:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nkhosa zanga zinasokera ku mapiri ali onse, ndi pa citunda ciri conse cacitali; inde nkhosa zanga zinabalalika pa dziko lonse lapansi, ndipo panalibe wakuzipwaira kapena kuzifunafuna.

Ezekieli 34

Ezekieli 34:1-10