Ezekieli 34:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zofoka simunazilimbitsa; yodwala simunaiciritsa, yotyoka simunailukira chika, yopitikitsidwa simunaibweza, yotayika simunaifuna; koma munazilamulira mwamphamvu ndi moopsa,

Ezekieli 34

Ezekieli 34:1-13