Ezekieli 34:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidzafuna yotayika, ndi kubweza yopitikitsidwa, ndi kulukira chika yotyoka mwendo, ndi kulimbitsa yodwalayo; koma yanenepa ndi yolimba ndidzaziononga, ndidzazidyetsa ndi ciweruzo.

Ezekieli 34

Ezekieli 34:12-18