Ezekieli 34:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Monga mbusa afunafuna nkhosa zace tsiku lokhala iye pakati pa nkhosa zace zobalalika, mamwemo ndidzafunafuna nkhosa zanga; ndipo ndidzawalanditsa m'malo monse anabalalikamo tsiku la mitambo ndi la mdima.

Ezekieli 34

Ezekieli 34:10-20