Ezekieli 33:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndikati Ine kwa woipa, Woipawe, udzafa ndithu, osanena iwe kumcenjeza woipayo aleke njira yace, woipa uyo adzafa m'mphulupulu yace, koma mwazi wace ndidzaufunsa pa dzanja lako.

Ezekieli 33

Ezekieli 33:7-17