Ezekieli 33:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova, posanduliza Ine dziko likhale lacipululu ndi lodabwitsa, cifukwa ca zonyansa zao zonse anazicita.

Ezekieli 33

Ezekieli 33:20-33