Ezekieli 33:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wobadwa ndi munthu iwe, iwo okhala ku mabwinja a dziko la Israyeli anena, ndi kuti, Abrahamu anali yekha, nakhala nalo dziko colowa cace; koma ife ndife ambiri, dzikoli lipatsidwa kwa ife colowa cathu.

Ezekieli 33

Ezekieli 33:16-32