Ezekieli 33:16-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

16. Zoipa zace ziri zonse anazicita sizidzakumbukika zimtsutse, anacita coyenera ndi colungama; adzakhala ndi moyo ndithu.

17. Koma ana a anthu a mtundu wako akuti, Njira ya Ambuye siiyenera; koma iwowa njira yao siiyenera.

18. Akabwerera wolungama kuleka cilungamo cace, nakacita cosalungama, adzafa m'mwemo.

Ezekieli 33