Ezekieli 33:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndikanena kwa wolungama kuti adzakhala ndi moyo ndithu, akatama cilungamo cace, akacita cosalungama, sizikumbukika zolungama zace ziri zonse; koma m'cosalungama cace anacicita momwemo adzafa.

Ezekieli 33

Ezekieli 33:4-20