Ezekieli 32:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidzagwetsa aunyinji ako ndi malupanga a eni mphamvu, ndiwo onse oopsetsa a amitundu; ndipo adzaipsa kudzikuza kwa Aigupto, ndi aunyinji ace onse adzaonongeka.

Ezekieli 32

Ezekieli 32:8-15