Ezekieli 31:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mbalame zonse za m'mlengalenga zinamanga zisa zao pa nthambi zace, ndi pansi pa nthawi zace zinaswana nyama zonse za kuthengo, ndi pa mthunzi wace inakhala mitundu yonse yaikuru ya anthu.

Ezekieli 31

Ezekieli 31:5-12