Ezekieli 30:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kusi, ndi Puti, ndi Ludi, ndi osokonezeka onse, ndi Kubi, ndi anthu a dziko lopangana nao, adzagwa pamodzi nao ndi lupanga.

Ezekieli 30

Ezekieli 30:3-8