Ezekieli 30:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzamwaza Aaigupto mwa amitundu, ndi kuwabalalitsa mwa amitundu; motero adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Ezekieli 30

Ezekieli 30:16-26