Ezekieli 30:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzalimbitsa manja a mfumu ya ku Babulo, ndi kuika lupanga langa m'dzanja lace; koma ndidzatyola manja a Parao, ndipo adzabuula pamaso pace mabuulo a munthu wopyozedwa.

Ezekieli 30

Ezekieli 30:16-26