Ezekieli 3:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

si kwa mitundu yambiri ya anthu a cinenedwe cosamveka ndi cobvuta, amene sukhoza kudziwitsa cinenedwe cao. Zedi ndikakutumiza kwa iwowa adzamvera iwe.

Ezekieli 3

Ezekieli 3:5-7