Ezekieli 3:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndidzamamatiritsa lilime lako ku malakalaka ako, kuti ukhale wosanena, wosawakhalira wakuwadzudzula; pakuti iwo ndiwo nyumba yopanduka.

Ezekieli 3

Ezekieli 3:16-27