Ezekieli 3:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinauka ndi kuturuka kumka kucidikha, ndipo taonani, ulemerero wa Yehova unaimako monga ulemerero uja ndinauona ku mtsinje Kebara, ndipo ndinagwa nkhope pansi.

Ezekieli 3

Ezekieli 3:13-27