Ezekieli 3:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ukamcenjeza wolungamayo, kuti asacimwe wolungamayo, ndipo sacimwa, adzakhala ndi moyo ndithu, popeza anacenjezedwa; ndipo iwe walanditsa moyo wako.

Ezekieli 3

Ezekieli 3:13-27