Ezekieli 29:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi dziko la Aigupto lidzakhala lopasuka ndi labwinja; ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova, popeza anati, Mtsinjewo ndi wanga, ndinaulenga ndine.

Ezekieli 29

Ezekieli 29:1-15