Ezekieli 28:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace taona, ndidzakufikitsira alendo oopsa a mitundu ya anthu, iwo adzasololera malupanga ao nzeru zako zokongola, nadzaipsa kunyezimira kwako.

Ezekieli 28

Ezekieli 28:5-14