Ezekieli 28:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Unadzikuza mtima cifukwa ca kukongola kwako, waipsa nzeru zako; cifukwa ca kuwala kwako ndakugwetsa pansi, ndakuika pamaso pa mafumu, kuti akupenye.

Ezekieli 28

Ezekieli 28:13-24