Ezekieli 27:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akr-ru a ku Gebala ndi eni luso ace anali mwa iwe kukonza ziboo zako; zombo zonse za kunyanja pamodzi ndi amarinyero ao anali mwa iwe kusinthana nawe malonda.

Ezekieli 27

Ezekieli 27:6-16