Ezekieli 27:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nadzamveketsa mau ao pa iwe, nadzalira mowawa mtima, nadzathira pfumbi pamitu pao, nadzakunkhulira m'maphulusa,

Ezekieli 27

Ezekieli 27:20-31