Ezekieli 26:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wobadwa ndi munthu iwe, popeza Turo ananyodola Yerusalemu, ndi kuti, Onyo, watyoka uwu udali cipata ca mitundu ya anthu; wanditembenukira ine; ndidzakhuta ine, wapasuka uwu;

Ezekieli 26

Ezekieli 26:1-6