Ezekieli 26:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo akalonga onse a kunyanja adzatsika ku mipando yacifumu yao, nadzabvula zobvala zao zopikapika, nadzabvala kunjenjemera, nadzakhala panthaka pansi, nadzanjenjemera mphindi zonse ndi kukudabwa.

Ezekieli 26

Ezekieli 26:15-21