Ezekieli 26:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzalanda cuma cako ndi kufunkha malonda ako, nadzagwetsa malinga ako ndi kupasula nyumba zako zofunika, nadzaponya miyala yako, ndi mitengo yako, ndi pfumbi lako, m'madzi.

Ezekieli 26

Ezekieli 26:4-13