Ezekieli 25:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzalibwezera Edomu cilango mwa dzanja la anthu anga Israyeli; ndipo adzacita m'Edomu monga mwa mkwiyo wanga, ndi ukali wanga; motero adzadziwa kubwezera cilango kwanga, ati Ambuye Yehova.

Ezekieli 25

Ezekieli 25:4-17