Ezekieli 24:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Usa moyo mosamveka, usalira wakufayo, dzimangire cilemba, nubvale nsapato ku mapazi ako, usaphimbe milomo yako, kapena kudya mkate wa anthu.

Ezekieli 24

Ezekieli 24:9-26