Ezekieli 23:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacita nao zigololo zace, ndiwo anthu osankhika a ku Asuri onsewo, ndipo ali onse anawaumirira anadziipsa nao mafano ao.

Ezekieli 23

Ezekieli 23:1-16