Ezekieli 23:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu olungama adzawaweruza monga mwa maweruzo a acigololo, ndi maweruzo a akazi okhetsa mwazi; pakuti ndiwo acigololo, ndi m'manja mwao muli mwazi.

Ezekieli 23

Ezekieli 23:36-49