Ezekieli 23:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso munatuma kuitana anthu ocokera kutali, ndiwo munawatumira mthenga; ndipo taona, anadza amenewo unasamba, cifukwa ca iwo unapaka maso ako mankhwala, ndi kubvala zokometsera;

Ezekieli 23

Ezekieli 23:35-48