Ezekieli 23:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti anacita cigololo, ndi m'manja mwao muli mwazi, ndipo anacita cigololo ndi mafano ao, nawapititsiranso pamoto ana ao amuna amene anandibalira, kuti athedwe.

Ezekieli 23

Ezekieli 23:30-41